Ambuye adzikudalitsani azimayi ife mmatidalitsa olo Uta khala ndi mavuto mtundu wanji nyimbo iyi imakuzizilitsa yan'gana kwa yesu ndiko kuli mtendere π
Iam from Finland l don't understand your language Malawian but l hope you people are enjoying the song makamaka apo akumati madzimaera yang'ana yang'ana π
Nyimbo ndikuyimva kukoma kwambiri Ngati Inunso Muyimva. Kukoma Like My Comment π₯±π₯±
ππ
Congratulations CCAP mwatulusako nyimbo yonvela ndi ma bar momwe
Mai anga like masitha continue rest in peace mama
β€My favorite song
π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯
Tonse akatolika omwe nyimboyi tayilandira ndi manja awiri tikumane pano
These women deserve awards
Song of the year
Me
ma moslem omse let's gather here β¦for the supportβ¦ayiphaa nyimboyii
Ife obadwila Ku kawale, tikumva kulemekezedwa heavy, regardless of denomination..love this tune!
Aimbe bwanji azimayiπ₯π₯π₯π₯π₯
Nyimbo iyiyi ngati sitenga ma award onse azanyimbo ndizayambitsa mademo dziko lonse
This song makes makes my day π’π
Best song of the year. Well done Masintha women. π₯³π₯³ππβ€β€β€β€
Koma nyimboyi mmmm azimayi wulemu wanu ndimangoyi beleza kuno mupa mabeba kukalipa
Song of the year ππ iyi yokha ward mwatenga Mai anga ku NANSADIko nyimbo ndiyomweyo
Olo kusintha mpingoko uyambira patiπππππ
nice.
The lead vocalist is the best
It reminds me my grandmother who use to sing at Msamaria RCZ chipata Congregation.Rest in piece Ambuya
Ambuye adzikudalitsani azimayi ife mmatidalitsa olo Uta khala ndi mavuto mtundu wanji nyimbo iyi imakuzizilitsa yan'gana kwa yesu ndiko kuli mtendere π
wa sda iwe pita uko ukuvera zaeni kkkk
Wangotsala mamuna wa sesepiππ
Masintha yadya 1β€
This song is very interesting β€β€like it @its very reactive like the group 1elements
Amene tikuyang'ana gather here
These can deliver. They never disappoint πππππ
This is the song of the year π₯³π₯³
Katundu wa boma
#Moffattung'ande
Choir iyiyi inabwera
Nyimbo imeneyi anakazinga zili bho azimay
that's right
Kawale on fire π₯
Masintha mumakwana
Very sweet. ,but I must get one there π π π
β€β€
moto moto masintha patsogolo ndi yesu mayi Dzozi Mayi kachitsa
Audio mpaka 1.3 million views
Iam from Finland l don't understand your language Malawian but l hope you people are enjoying the song makamaka apo akumati madzimaera yang'ana yang'ana π
Ife kudalitsika zedi za mphamvu izi
Za voice tikambabe koma whoβs here with me saluting the producer?β
Instrumental yaphedwa iyi.
By the way, uziki iyiyi yabwera msangatu. Bwenzi ikutuluka cha mβ ma 20 satemu.
Nyimbo yabwino uiwala mavhuto onse
azimayi mwalusa kuimba ngat kulibe mawaaa
ππππΏπ²πΏπ²
Kwa Yesu kuli umoyo
β€β€ππππππ
Gogogo Masintha. Amennnnn
nyimbo ilibwino iyi yang'ana yang'ana
vj Ice